Yohane 21:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Zitatero, wophunzira amene Yesu anali kumukonda kwambiri uja+ anauza Petulo+ kuti: “Ndi Ambuye!” Pamenepo Simoni Petulo atamva kuti ndi Ambuye, anavala malaya ake ovala pamwamba, pakuti anali maliseche,* ndipo analumphira m’nyanja.
7 Zitatero, wophunzira amene Yesu anali kumukonda kwambiri uja+ anauza Petulo+ kuti: “Ndi Ambuye!” Pamenepo Simoni Petulo atamva kuti ndi Ambuye, anavala malaya ake ovala pamwamba, pakuti anali maliseche,* ndipo analumphira m’nyanja.