Mateyu 14:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 ndipo anauza atumiki ake kuti: “Ameneyu ndi Yohane M’batizi. Anauka kwa akufa, ndipo n’chifukwa chake akuchita ntchito zamphamvu.”+ Luka 9:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Tsopano Herode* wolamulira chigawo anamva zonse zimene zinali kuchitika. Iye anathedwa nzeru chifukwa ena anali kunena kuti Yohane anauka kwa akufa.+
2 ndipo anauza atumiki ake kuti: “Ameneyu ndi Yohane M’batizi. Anauka kwa akufa, ndipo n’chifukwa chake akuchita ntchito zamphamvu.”+
7 Tsopano Herode* wolamulira chigawo anamva zonse zimene zinali kuchitika. Iye anathedwa nzeru chifukwa ena anali kunena kuti Yohane anauka kwa akufa.+