Maliko 8:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Pamenepo anawaletsa mwamphamvu kuti asauze aliyense za iye.+ Luka 9:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndiyeno anawalangiza mwamphamvu kuti asauze aliyense zimenezo.+