Mateyu 16:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Pamenepo analamula ophunzirawo mwamphamvu kuti asauze aliyense kuti iye ndi Khristu.+ Maliko 9:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pamene anali kutsika m’phirimo, Yesu anawalangiza mwamphamvu kuti asauze+ aliyense zimene anaonazo, kufikira Mwana wa munthu atauka kwa akufa.+ Luka 9:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndiyeno anawalangiza mwamphamvu kuti asauze aliyense zimenezo.+
9 Pamene anali kutsika m’phirimo, Yesu anawalangiza mwamphamvu kuti asauze+ aliyense zimene anaonazo, kufikira Mwana wa munthu atauka kwa akufa.+