Mateyu 17:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pamene anali kutsika m’phirimo, Yesu anawalamula kuti: “Musauze wina aliyense za masomphenya amenewa kufikira Mwana wa munthu ataukitsidwa kwa akufa.”+ Luka 9:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Pamene mawuwo anali kumveka, anaona kuti Yesu ali yekha.+ Koma iwo anakhala chete ndipo sanauze aliyense m’masiku amenewo chilichonse mwa zimene anaonazo.+
9 Pamene anali kutsika m’phirimo, Yesu anawalamula kuti: “Musauze wina aliyense za masomphenya amenewa kufikira Mwana wa munthu ataukitsidwa kwa akufa.”+
36 Pamene mawuwo anali kumveka, anaona kuti Yesu ali yekha.+ Koma iwo anakhala chete ndipo sanauze aliyense m’masiku amenewo chilichonse mwa zimene anaonazo.+