Mateyu 17:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pamene anali kutsika m’phirimo, Yesu anawalamula kuti: “Musauze wina aliyense za masomphenya amenewa kufikira Mwana wa munthu ataukitsidwa kwa akufa.”+ Maliko 9:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pamene anali kutsika m’phirimo, Yesu anawalangiza mwamphamvu kuti asauze+ aliyense zimene anaonazo, kufikira Mwana wa munthu atauka kwa akufa.+
9 Pamene anali kutsika m’phirimo, Yesu anawalamula kuti: “Musauze wina aliyense za masomphenya amenewa kufikira Mwana wa munthu ataukitsidwa kwa akufa.”+
9 Pamene anali kutsika m’phirimo, Yesu anawalangiza mwamphamvu kuti asauze+ aliyense zimene anaonazo, kufikira Mwana wa munthu atauka kwa akufa.+