Mateyu 16:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Pamenepo analamula ophunzirawo mwamphamvu kuti asauze aliyense kuti iye ndi Khristu.+ Maliko 8:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Pamenepo anawaletsa mwamphamvu kuti asauze aliyense za iye.+