Luka 15:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Akafika kunyumba amasonkhanitsa mabwenzi ake ndi anthu oyandikana naye n’kuwauza kuti, ‘Kondwerani nane limodzi, chifukwa ndapeza nkhosa yanga imene inatayika ija.’+
6 Akafika kunyumba amasonkhanitsa mabwenzi ake ndi anthu oyandikana naye n’kuwauza kuti, ‘Kondwerani nane limodzi, chifukwa ndapeza nkhosa yanga imene inatayika ija.’+