Deuteronomo 24:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 “Mwamuna akatenga mkazi kuti akhale mkazi wake, ndiyeno ngati mkaziyo sanamusangalatse chifukwa wam’peza ndi vuto linalake,+ azimulembera kalata yothetsera ukwati+ ndi kum’patsa m’manja mwake, n’kumuchotsa panyumba pake.+ Mateyu 5:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 “Pajanso anati, ‘Aliyense wothetsa ukwati+ ndi mkazi wake, apatse mkaziyo kalata yothetsera ukwati.’+
24 “Mwamuna akatenga mkazi kuti akhale mkazi wake, ndiyeno ngati mkaziyo sanamusangalatse chifukwa wam’peza ndi vuto linalake,+ azimulembera kalata yothetsera ukwati+ ndi kum’patsa m’manja mwake, n’kumuchotsa panyumba pake.+
31 “Pajanso anati, ‘Aliyense wothetsa ukwati+ ndi mkazi wake, apatse mkaziyo kalata yothetsera ukwati.’+