Luka 18:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Ndiyeno amene anali patsogolo anayamba kumudzudzula mwamphamvu kuti akhale chete. Koma m’pamenenso iye anafuula kwambiri kuti: “Mwana wa Davide, ndichitireni chifundo.”+
39 Ndiyeno amene anali patsogolo anayamba kumudzudzula mwamphamvu kuti akhale chete. Koma m’pamenenso iye anafuula kwambiri kuti: “Mwana wa Davide, ndichitireni chifundo.”+