Mateyu 20:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Pamenepo khamu la anthulo linawakalipira kuti akhale chete, koma m’pamene anafuula kwambiri kuti: “Ambuye, Mwana wa Davide, tichitireni chifundo!”+ Maliko 10:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Pamene ambiri anali kumuuza mwamphamvu kuti akhale chete, m’pamenenso iye anafuula kwambiri kuti: “Mwana wa Davide, ndichitireni chifundo!”+
31 Pamenepo khamu la anthulo linawakalipira kuti akhale chete, koma m’pamene anafuula kwambiri kuti: “Ambuye, Mwana wa Davide, tichitireni chifundo!”+
48 Pamene ambiri anali kumuuza mwamphamvu kuti akhale chete, m’pamenenso iye anafuula kwambiri kuti: “Mwana wa Davide, ndichitireni chifundo!”+