Mateyu 20:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Pamenepo khamu la anthulo linawakalipira kuti akhale chete, koma m’pamene anafuula kwambiri kuti: “Ambuye, Mwana wa Davide, tichitireni chifundo!”+ Luka 18:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Ndiyeno amene anali patsogolo anayamba kumudzudzula mwamphamvu kuti akhale chete. Koma m’pamenenso iye anafuula kwambiri kuti: “Mwana wa Davide, ndichitireni chifundo.”+
31 Pamenepo khamu la anthulo linawakalipira kuti akhale chete, koma m’pamene anafuula kwambiri kuti: “Ambuye, Mwana wa Davide, tichitireni chifundo!”+
39 Ndiyeno amene anali patsogolo anayamba kumudzudzula mwamphamvu kuti akhale chete. Koma m’pamenenso iye anafuula kwambiri kuti: “Mwana wa Davide, ndichitireni chifundo.”+