Yesaya 40:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Tamverani! Winawake akufuula m’chipululu kuti:+ “Konzani njira ya Yehova+ anthu inu! Wongolani msewu wa Mulungu wathu wodutsa m’chipululu.+ Luka 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Anali kuchita zimenezi monga mmene analembera m’buku la mawu a Yesaya mneneri kuti: “Tamverani! Winawake akufuula m’chipululu kuti, ‘Konzani njira ya Yehova anthu inu! Wongolani misewu yake.+ Yohane 1:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Iye anati: “Ndine mawu a winawake wofuula m’chipululu kuti, ‘Wongolani njira ya Yehova,’ monga mmene mneneri Yesaya ananenera.”+
3 Tamverani! Winawake akufuula m’chipululu kuti:+ “Konzani njira ya Yehova+ anthu inu! Wongolani msewu wa Mulungu wathu wodutsa m’chipululu.+
4 Anali kuchita zimenezi monga mmene analembera m’buku la mawu a Yesaya mneneri kuti: “Tamverani! Winawake akufuula m’chipululu kuti, ‘Konzani njira ya Yehova anthu inu! Wongolani misewu yake.+
23 Iye anati: “Ndine mawu a winawake wofuula m’chipululu kuti, ‘Wongolani njira ya Yehova,’ monga mmene mneneri Yesaya ananenera.”+