Mateyu 13:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pa nthawiyo anawauza zinthu zambiri mwa mafanizo kuti: “Tamverani! Wofesa mbewu anapita kukafesa mbewu.+ Maliko 12:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Pophunzitsapo Yesu ananenanso kuti: “Chenjerani ndi alembi+ amene amakonda kuyendayenda atavala mikanjo ndi kupatsidwa moni m’misika.
3 Pa nthawiyo anawauza zinthu zambiri mwa mafanizo kuti: “Tamverani! Wofesa mbewu anapita kukafesa mbewu.+
38 Pophunzitsapo Yesu ananenanso kuti: “Chenjerani ndi alembi+ amene amakonda kuyendayenda atavala mikanjo ndi kupatsidwa moni m’misika.