Mateyu 13:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma dzuwa litakwera zinawauka, ndipo chifukwa chopanda mizu zinafota.+ Yakobo 1:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Dzuwa limatuluka ndi kutentha kwake n’kufotetsa zomera, ndipo maluwa a zomerazo amathothoka. Kukongola kwake kumatha. Momwemonso munthu wachuma adzafa akutsatira njira ya moyo wake.+
11 Dzuwa limatuluka ndi kutentha kwake n’kufotetsa zomera, ndipo maluwa a zomerazo amathothoka. Kukongola kwake kumatha. Momwemonso munthu wachuma adzafa akutsatira njira ya moyo wake.+