Mateyu 13:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Koma zofesedwa pamiyala, ndi munthu amene wamva mawu ndi kuwavomereza mwamsanga ndiponso mwachimwemwe.+ Mateyu 13:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Komabe pa iye yekha alibe mizu ndipo amapitirizabe kwa kanthawi. Koma pamene chisautso kapena mazunzo zayamba chifukwa cha mawuwo, iye amapunthwa mwamsanga.+ Maliko 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma dzuwa litakwera, mbewuzo zinawauka ndipo popeza zinalibe mizu zinafota.+
20 Koma zofesedwa pamiyala, ndi munthu amene wamva mawu ndi kuwavomereza mwamsanga ndiponso mwachimwemwe.+
21 Komabe pa iye yekha alibe mizu ndipo amapitirizabe kwa kanthawi. Koma pamene chisautso kapena mazunzo zayamba chifukwa cha mawuwo, iye amapunthwa mwamsanga.+