Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 58:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Koma tsiku ndi tsiku iwo anali kufunafuna ineyo. Anali kunena kuti amasangalala kudziwa njira zanga,+ ngati mtundu umene unali kuchita zolungama ndiponso ngati mtundu umene sunasiye chilungamo cha Mulungu wawo.+ Iwo ankangokhalira kundipempha chiweruzo cholungama, ndipo anali kuyandikira kwa Mulungu amene anali kumukonda.+

  • Ezekieli 33:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Iwo adzabwera kwa iwe ngati mmene amachitira nthawi zonse ndipo adzakhala pamaso pako ngati anthu anga.+ Adzamva mawu ako koma sadzawatsatira,+ chifukwa ndi pakamwa pawo, akulankhula za zilakolako zawo zonyansa ndipo mtima wawo uli pa kupeza phindu mopanda chilungamo.+

  • Yohane 5:35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 Munthu ameneyu anali nyale yoyaka ndi yowala, ndipo kwa kanthawi kochepa inu munali ofunitsitsa kusangalala m’kuwala kwakeko.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena