Miyambo 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Munthu wanzeru amamvetsera ndi kuphunzira malangizo owonjezereka,+ ndipo munthu womvetsa zinthu ndi amene amapeza nzeru zoyendetsera moyo wake,+ Mateyu 11:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Amene ali ndi makutu amve.+ Chivumbulutso 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ali ndi makutu amve zimene mzimu+ ukunena ku mipingo kuti: Wopambana pa nkhondo,+ ndidzamulola kudya za mumtengo wa moyo,+ umene uli m’paradaiso wa Mulungu.’
5 Munthu wanzeru amamvetsera ndi kuphunzira malangizo owonjezereka,+ ndipo munthu womvetsa zinthu ndi amene amapeza nzeru zoyendetsera moyo wake,+
7 Ali ndi makutu amve zimene mzimu+ ukunena ku mipingo kuti: Wopambana pa nkhondo,+ ndidzamulola kudya za mumtengo wa moyo,+ umene uli m’paradaiso wa Mulungu.’