Salimo 104:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Zolengedwa zouluka m’mlengalenga zimamanga zisa zawo pafupi ndi akasupewo,+Ndipo zimalira m’mitengo ya masamba ambiri obiriwira.+ Ezekieli 31:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Zolengedwa zonse zouluka m’mlengalenga zinali kumanga zisa zawo m’nthambi zake zikuluzikuluzo.+ Nyama zonse zakutchire zinkaberekera pansi pa nthambi zake.+ Mitundu yonse ya anthu ambiri inali kukhala mumthunzi wake.
12 Zolengedwa zouluka m’mlengalenga zimamanga zisa zawo pafupi ndi akasupewo,+Ndipo zimalira m’mitengo ya masamba ambiri obiriwira.+
6 Zolengedwa zonse zouluka m’mlengalenga zinali kumanga zisa zawo m’nthambi zake zikuluzikuluzo.+ Nyama zonse zakutchire zinkaberekera pansi pa nthambi zake.+ Mitundu yonse ya anthu ambiri inali kukhala mumthunzi wake.