Mateyu 8:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Kenako panyanjapo panabuka mphepo yamphamvu moti mafunde anali kulowa m’ngalawamo, koma iye anali m’tulo.+ Luka 8:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Koma ulendowo uli mkati Yesu anagona tulo. Kenako panyanjapo panayamba kuwomba mphepo yamkuntho, ndipo madzi anayamba kudzaza m’ngalawamo moti akanatha kumira.+
24 Kenako panyanjapo panabuka mphepo yamphamvu moti mafunde anali kulowa m’ngalawamo, koma iye anali m’tulo.+
23 Koma ulendowo uli mkati Yesu anagona tulo. Kenako panyanjapo panayamba kuwomba mphepo yamkuntho, ndipo madzi anayamba kudzaza m’ngalawamo moti akanatha kumira.+