Mateyu 8:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Kenako panyanjapo panabuka mphepo yamphamvu moti mafunde anali kulowa m’ngalawamo, koma iye anali m’tulo.+ Maliko 4:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Kenako kunayamba chimphepo champhamvu chamkuntho, ndipo mafunde anali kuwomba ngalawayo, mwakuti ngalawayo inangotsala pang’ono kumira.+
24 Kenako panyanjapo panabuka mphepo yamphamvu moti mafunde anali kulowa m’ngalawamo, koma iye anali m’tulo.+
37 Kenako kunayamba chimphepo champhamvu chamkuntho, ndipo mafunde anali kuwomba ngalawayo, mwakuti ngalawayo inangotsala pang’ono kumira.+