Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 8:34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 Zitatero, anthu onse mumzindawo anapita kukakumana ndi Yesu. Atamuona, anam’pempha kuti achoke m’madera akwawoko.+

  • Luka 8:37
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 37 Choncho khamu lonse lochokera m’midzi yapafupi ya Agerasa linam’pempha kuti achoke kwawoko, chifukwa linagwidwa ndi mantha aakulu.+ Pamenepo iye anakwera ngalawa kuti azipita.

  • Machitidwe 16:39
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 39 Chotero anabwera ndi kuwachonderera, ndipo atawatulutsa anawapempha kuti achoke mumzindawo.

  • 1 Akorinto 2:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Koma munthu wokonda zinthu za m’dziko* salandira zinthu za mzimu wa Mulungu, chifukwa amaziona ngati zopusa ndipo sangathe kuzidziwa,+ chifukwa zimafuna kuzifufuza mwauzimu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena