Luka 8:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Kenako panafika munthu wina dzina lake Yairo. Iyeyu anali mtsogoleri wa sunagoge. Ndiyeno anadzigwetsa pamapazi a Yesu ndi kum’chonderera kuti akalowe m’nyumba yake.+
41 Kenako panafika munthu wina dzina lake Yairo. Iyeyu anali mtsogoleri wa sunagoge. Ndiyeno anadzigwetsa pamapazi a Yesu ndi kum’chonderera kuti akalowe m’nyumba yake.+