Mateyu 9:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pamene anali kuwauza zimenezi, wolamulira wina+ anam’yandikira. Kenako anamugwadira+ n’kunena kuti: “Panopa mwana wanga wamkazi ayenera kuti wamwalira kale.+ Koma tiyeni mukamukhudze ndi dzanja lanu ndipo akhala ndi moyo.”+ Maliko 5:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pamenepo mmodzi wa atsogoleri a sunagoge, dzina lake Yairo, anafika. Atamuona anagwada pamapazi ake+
18 Pamene anali kuwauza zimenezi, wolamulira wina+ anam’yandikira. Kenako anamugwadira+ n’kunena kuti: “Panopa mwana wanga wamkazi ayenera kuti wamwalira kale.+ Koma tiyeni mukamukhudze ndi dzanja lanu ndipo akhala ndi moyo.”+
22 Pamenepo mmodzi wa atsogoleri a sunagoge, dzina lake Yairo, anafika. Atamuona anagwada pamapazi ake+