Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Maliko 6:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Chotero sanathe kuchita ntchito zamphamvu zilizonse kumeneko, koma anangoika manja pa odwala owerengeka ndi kuwachiritsa.

  • Luka 4:40
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 40 Koma pamene dzuwa linali kulowa, onse amene anali ndi anthu odwala matenda osiyanasiyana anawabweretsa kwa iye. Ndipo iye anawachiritsa mwa kuika manja ake pa aliyense.+

  • Machitidwe 9:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Choncho Hananiya anapita ndi kukalowa m’nyumbamo. Ndiyeno anamuika manja n’kunena kuti: “M’bale wanga Saulo, Ambuye Yesu amene waonekera kwa iwe pamsewu umene wadzera, wandituma ine. Wandituma kwa iwe kuti uyambenso kuona ndi kutinso udzazidwe ndi mzimu woyera.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena