Mlaliki 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Awiri amaposa mmodzi,+ chifukwa amapeza mphoto yabwino pa ntchito yawo imene amaigwira mwakhama.+ Luka 10:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pambuyo pake, Ambuye anasankha anthu ena 70+ ndi kuwatumiza awiriawiri+ kuti atsogole kupita mumzinda ndi malo alionse kumene iye adzafikeko.
10 Pambuyo pake, Ambuye anasankha anthu ena 70+ ndi kuwatumiza awiriawiri+ kuti atsogole kupita mumzinda ndi malo alionse kumene iye adzafikeko.