Ekisodo 24:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Choncho Mulungu anauza Mose kuti: “Kwera upite kwa Yehova, iweyo, Aroni, Nadabu, Abihu+ ndi akulu 70+ a Isiraeli, ndipo mugwade chapatali. Numeri 11:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndiyeno Yehova anauza Mose kuti: “Undisonkhanitsire akulu 70 mwa akulu a Isiraeli,+ amene ukuwadziwa kuti ndiwo akulu ndi oyang’anira pakati pa anthuwo.+ Upite nawo kuchihema chokumanako, ndipo akaime kumeneko limodzi nawe.
24 Choncho Mulungu anauza Mose kuti: “Kwera upite kwa Yehova, iweyo, Aroni, Nadabu, Abihu+ ndi akulu 70+ a Isiraeli, ndipo mugwade chapatali.
16 Ndiyeno Yehova anauza Mose kuti: “Undisonkhanitsire akulu 70 mwa akulu a Isiraeli,+ amene ukuwadziwa kuti ndiwo akulu ndi oyang’anira pakati pa anthuwo.+ Upite nawo kuchihema chokumanako, ndipo akaime kumeneko limodzi nawe.