Levitiko 10:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndiyeno Nadabu ndi Abihu,+ ana a Aroni, aliyense anatenga chofukizira,+ n’kuikamo moto ndi zofukiza+ pamwamba pake. Pamenepo anayamba kupereka zofukiza pamoto wosaloledwa+ ndi Yehova, umene iye sanawalamule. 1 Mbiri 6:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ana a Amuramu+ anali Aroni,+ Mose,+ ndi Miriamu.+ Ana a Aroni anali Nadabu,+ Abihu,+ Eleazara,+ ndi Itamara.+
10 Ndiyeno Nadabu ndi Abihu,+ ana a Aroni, aliyense anatenga chofukizira,+ n’kuikamo moto ndi zofukiza+ pamwamba pake. Pamenepo anayamba kupereka zofukiza pamoto wosaloledwa+ ndi Yehova, umene iye sanawalamule.
3 Ana a Amuramu+ anali Aroni,+ Mose,+ ndi Miriamu.+ Ana a Aroni anali Nadabu,+ Abihu,+ Eleazara,+ ndi Itamara.+