Mateyu 4:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Komanso atachoka ku Nazareti, anafika ku Kaperenao+ n’kupeza malo okhala m’mphepete mwa nyanja m’zigawo za Zebuloni ndi Nafitali,+ Luka 4:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Choncho anapita ku Kaperenao,+ mzinda wa ku Galileya. Ndipo anali kuwaphunzitsa pa sabata.
13 Komanso atachoka ku Nazareti, anafika ku Kaperenao+ n’kupeza malo okhala m’mphepete mwa nyanja m’zigawo za Zebuloni ndi Nafitali,+