Machitidwe 2:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Petulo anawayankha kuti: “Lapani,+ ndipo aliyense wa inu abatizidwe+ m’dzina+ la Yesu Khristu kuti machimo anu akhululukidwe.+ Mukatero mudzalandira mphatso yaulere+ ya mzimu woyera. Machitidwe 3:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 “Chotero lapani+ ndi kutembenuka+ kuti machimo anu afafanizidwe,+ ndiponso kuti nyengo zotsitsimutsa+ zibwere kuchokera kwa Yehova.
38 Petulo anawayankha kuti: “Lapani,+ ndipo aliyense wa inu abatizidwe+ m’dzina+ la Yesu Khristu kuti machimo anu akhululukidwe.+ Mukatero mudzalandira mphatso yaulere+ ya mzimu woyera.
19 “Chotero lapani+ ndi kutembenuka+ kuti machimo anu afafanizidwe,+ ndiponso kuti nyengo zotsitsimutsa+ zibwere kuchokera kwa Yehova.