Luka 10:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Tsopano anthu okwana 70 aja anabwerera ali osangalala. Iwo anauza Yesu kuti: “Ambuye, ngakhale ziwanda zinatigonjera+ pamene tinagwiritsa ntchito dzina lanu.”
17 Tsopano anthu okwana 70 aja anabwerera ali osangalala. Iwo anauza Yesu kuti: “Ambuye, ngakhale ziwanda zinatigonjera+ pamene tinagwiritsa ntchito dzina lanu.”