Mateyu 14:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Koma nthawi yomweyo Yesu anawauza kuti: “Limbani mtima, ndine.+ Musachite mantha.” Yohane 6:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndiyeno Yesu anawauza kuti: “Ndine, musachite mantha!”+