Mateyu 14:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Koma nthawi yomweyo Yesu anawauza kuti: “Limbani mtima, ndine.+ Musachite mantha.” Maliko 6:50 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 50 Anachita zimenezi chifukwa onsewo anamuona ndipo anavutika mumtima. Koma nthawi yomweyo iye analankhula nawo, kuti: “Limbani mtima, ndine musachite mantha.”+
50 Anachita zimenezi chifukwa onsewo anamuona ndipo anavutika mumtima. Koma nthawi yomweyo iye analankhula nawo, kuti: “Limbani mtima, ndine musachite mantha.”+