Maliko 6:50 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 50 Anachita zimenezi chifukwa onsewo anamuona ndipo anavutika mumtima. Koma nthawi yomweyo iye analankhula nawo, kuti: “Limbani mtima, ndine musachite mantha.”+ Yohane 6:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndiyeno Yesu anawauza kuti: “Ndine, musachite mantha!”+ Machitidwe 23:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma tsiku lomwelo usiku, Ambuye anaimirira pambali pake+ ndi kunena kuti: “Limba mtima!+ Pakuti wandichitira umboni mokwanira+ mu Yerusalemu, ndipo ukandichitiranso umboni ku Roma.”+
50 Anachita zimenezi chifukwa onsewo anamuona ndipo anavutika mumtima. Koma nthawi yomweyo iye analankhula nawo, kuti: “Limbani mtima, ndine musachite mantha.”+
11 Koma tsiku lomwelo usiku, Ambuye anaimirira pambali pake+ ndi kunena kuti: “Limba mtima!+ Pakuti wandichitira umboni mokwanira+ mu Yerusalemu, ndipo ukandichitiranso umboni ku Roma.”+