Mateyu 9:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Tsopano pamene iwo anali kunyamuka, anthu anam’bweretsera munthu wosalankhula wogwidwa ndi chiwanda.+ Luka 11:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Nthawi inayake anali kutulutsa chiwanda cholepheretsa munthu kulankhula.+ Chiwandacho chitatuluka, munthu wosalankhulayo analankhula, ndipo khamu la anthu linadabwa kwambiri. Machitidwe 9:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 ndipo m’masomphenya waona munthu dzina lake Hananiya, amene anafika ndi kumuika manja kuti ayambenso kuona.”+
32 Tsopano pamene iwo anali kunyamuka, anthu anam’bweretsera munthu wosalankhula wogwidwa ndi chiwanda.+
14 Nthawi inayake anali kutulutsa chiwanda cholepheretsa munthu kulankhula.+ Chiwandacho chitatuluka, munthu wosalankhulayo analankhula, ndipo khamu la anthu linadabwa kwambiri.
12 ndipo m’masomphenya waona munthu dzina lake Hananiya, amene anafika ndi kumuika manja kuti ayambenso kuona.”+