Yesaya 35:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pa nthawi imeneyo, maso a anthu akhungu adzatsegulidwa,+ ndipo makutu a anthu ogontha adzayamba kumva.+ Mateyu 15:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Khamu la anthulo linadabwa kuona osalankhula akulankhula, olumala akuyenda ndiponso akhungu akuona, ndipo anatamanda Mulungu wa Isiraeli.+
5 Pa nthawi imeneyo, maso a anthu akhungu adzatsegulidwa,+ ndipo makutu a anthu ogontha adzayamba kumva.+
31 Khamu la anthulo linadabwa kuona osalankhula akulankhula, olumala akuyenda ndiponso akhungu akuona, ndipo anatamanda Mulungu wa Isiraeli.+