Mateyu 16:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Nanga bwanji simukuzindikira kuti sindikunena za mitanda ya mkate? Koma samalani ndi zofufumitsa za Afarisi ndi Asaduki.”+ Maliko 6:52 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 52 Popeza sanamvetse tanthauzo la mitanda ya mkate ija, mitima yawo inakhalabe yosazindikira.+
11 Nanga bwanji simukuzindikira kuti sindikunena za mitanda ya mkate? Koma samalani ndi zofufumitsa za Afarisi ndi Asaduki.”+