Levitiko 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “‘Nsembe yambewu imene mudzapereka kwa Yehova ikhale yopanda chofufumitsa,+ chifukwa simuyenera kutentha mtanda wofufumitsa wa ufa wokanda ndiponso uchi,* monga nsembe yotentha ndi moto yoperekedwa kwa Yehova. Levitiko 6:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pophika, musaikemo chofufumitsa chilichonse.+ Ndaupereka monga gawo lawo kuchokera pansembe zanga zotentha ndi moto.+ Zimenezi n’zopatulika+ koposa mofanana ndi nsembe yamachimo ndi nsembe ya kupalamula. Maliko 8:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Pamenepo iye anawafunsa kuti: “Kodi simukumvetsabe tanthauzo lake?”+ Luka 12:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pa nthawiyi, chikhamu cha anthu masauzandemasauzande chinali chitasonkhana, moti anali kupondanapondana. Pamenepo Yesu anayamba kulankhula ndi ophunzira ake choyamba kuti: “Samalani ndi chofufumitsa+ cha Afarisi, chimene chili chinyengo.+
11 “‘Nsembe yambewu imene mudzapereka kwa Yehova ikhale yopanda chofufumitsa,+ chifukwa simuyenera kutentha mtanda wofufumitsa wa ufa wokanda ndiponso uchi,* monga nsembe yotentha ndi moto yoperekedwa kwa Yehova.
17 Pophika, musaikemo chofufumitsa chilichonse.+ Ndaupereka monga gawo lawo kuchokera pansembe zanga zotentha ndi moto.+ Zimenezi n’zopatulika+ koposa mofanana ndi nsembe yamachimo ndi nsembe ya kupalamula.
12 Pa nthawiyi, chikhamu cha anthu masauzandemasauzande chinali chitasonkhana, moti anali kupondanapondana. Pamenepo Yesu anayamba kulankhula ndi ophunzira ake choyamba kuti: “Samalani ndi chofufumitsa+ cha Afarisi, chimene chili chinyengo.+