Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 12:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Musamadzapezeke mtanda wa ufa wokanda wokhala ndi chofufumitsa m’nyumba zanu kwa masiku 7, chifukwa aliyense wakudya mtanda wokhala ndi chofufumitsa, kaya ndi mlendo kapena mbadwa ya Isiraeli,+ munthu ameneyo adzaphedwa kuti asakhalenso mu khamu la Isiraeli.+

  • Levitiko 6:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Pophika, musaikemo chofufumitsa chilichonse.+ Ndaupereka monga gawo lawo kuchokera pansembe zanga zotentha ndi moto.+ Zimenezi n’zopatulika+ koposa mofanana ndi nsembe yamachimo ndi nsembe ya kupalamula.

  • Mateyu 16:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Pamenepo anazindikira kuti sakunena kuti asamale ndi zofufumitsa mitanda ya mkate, koma kuti asamale ndi zimene Afarisi ndi Asaduki amaphunzitsa.+

  • 1 Akorinto 5:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Chotsani chofufumitsa chakalecho, kuti mukhale mtanda watsopano,+ popeza ndinu opanda chofufumitsa. Pakuti Khristu+ waperekedwa+ monga nsembe yathu ya pasika.+

  • Agalatiya 5:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Chofufumitsa chaching’ono chimafufumitsa mtanda wonse.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena