Mateyu 8:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndiyeno Yesu anamuuza kuti: “Samala, usauze aliyense zimenezi,+ koma upite ukadzionetse kwa wansembe,+ ndipo ukapereke mphatso+ imene Mose analamula, kuti ikhale umboni kwa iwo.” Maliko 5:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Koma iye anawalamula mobwerezabwereza kuti asauze aliyense zimenezi.+ Kenako anawauza kuti apatse mtsikanayo chakudya.
4 Ndiyeno Yesu anamuuza kuti: “Samala, usauze aliyense zimenezi,+ koma upite ukadzionetse kwa wansembe,+ ndipo ukapereke mphatso+ imene Mose analamula, kuti ikhale umboni kwa iwo.”
43 Koma iye anawalamula mobwerezabwereza kuti asauze aliyense zimenezi.+ Kenako anawauza kuti apatse mtsikanayo chakudya.