2 Mafumu 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iwo anayankha kuti: “Munthuyo anavala chovala chaubweya+ ndi lamba wachikopa m’chiuno mwake.”+ Mfumuyo itangomva zimenezi, inanena kuti: “Ndi Eliya wa ku Tisibe.”
8 Iwo anayankha kuti: “Munthuyo anavala chovala chaubweya+ ndi lamba wachikopa m’chiuno mwake.”+ Mfumuyo itangomva zimenezi, inanena kuti: “Ndi Eliya wa ku Tisibe.”