Mateyu 17:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ataona izi, Petulo anauza Yesu kuti: “Ambuye, ndi bwino ife tizikhala pano. Ngati mukufuna, ndimanga mahema atatu pano, limodzi lanu, limodzi la Mose ndi lina la Eliya.”+ Luka 9:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Tsopano pamene amenewa anali kulekana naye, Petulo anauza Yesu kuti:+ “Mlangizi, ndi bwino kuti ife tizikhala pano. Choncho timange mahema atatu, limodzi lanu, limodzi la Mose ndi lina la Eliya.” Koma iye sanali kuzindikira zimene anali kunena.
4 Ataona izi, Petulo anauza Yesu kuti: “Ambuye, ndi bwino ife tizikhala pano. Ngati mukufuna, ndimanga mahema atatu pano, limodzi lanu, limodzi la Mose ndi lina la Eliya.”+
33 Tsopano pamene amenewa anali kulekana naye, Petulo anauza Yesu kuti:+ “Mlangizi, ndi bwino kuti ife tizikhala pano. Choncho timange mahema atatu, limodzi lanu, limodzi la Mose ndi lina la Eliya.” Koma iye sanali kuzindikira zimene anali kunena.