Genesis 1:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Motero Mulungu analenga munthu m’chifaniziro chake,+ m’chifaniziro cha Mulungu anam’lenga iye. Anawalenga mwamuna ndi mkazi.+ Genesis 5:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Anawalenga iwo mwamuna ndi mkazi.+ Kenako, anawadalitsa ndi kuwatchula dzina lakuti Anthu,+ m’tsiku limene anawalenga.+ Mateyu 19:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Yesu anayankha kuti: “Kodi simunawerenge kuti amene analenga anthu pa chiyambi pomwe anawalenga mwamuna ndi mkazi+
27 Motero Mulungu analenga munthu m’chifaniziro chake,+ m’chifaniziro cha Mulungu anam’lenga iye. Anawalenga mwamuna ndi mkazi.+
2 Anawalenga iwo mwamuna ndi mkazi.+ Kenako, anawadalitsa ndi kuwatchula dzina lakuti Anthu,+ m’tsiku limene anawalenga.+
4 Yesu anayankha kuti: “Kodi simunawerenge kuti amene analenga anthu pa chiyambi pomwe anawalenga mwamuna ndi mkazi+