Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 7:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Chotero zamoyo zonse zoyenda padziko lapansi, monga zolengedwa zouluka, nyama zoweta, nyama zakutchire, ndiponso tizilombo tonse tambirimbiri toyenda padziko lapansi, zinafa+ pamodzi ndi anthu onse.+

  • Mlaliki 3:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Ndani akudziwa ngati mzimu* wa ana a anthu umakwera m’mwamba, ndiponso ngati mzimu wa zinyama umatsika pansi?+

  • Machitidwe 17:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Zoona, Mulungu analekerera nthawi ya kusadziwa koteroko,+ koma tsopano akuuza anthu kwina kulikonse kuti onse alape.+

  • 1 Akorinto 15:39
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 39 Mnofu sukhala wa mtundu umodzi, koma pali mnofu wa munthu, ndipo pali wa nyama, palinso wa mbalame, ndi winanso wa nsomba.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena