Mateyu 18:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Chotero, aliyense amene adzadzichepetsa+ ngati mwana wamng’ono uyu ndi amene adzakhala wamkulu kwambiri mu ufumu wakumwamba.+ Mateyu 19:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma Yesu anawauza kuti: “Alekeni anawo, ndipo musawaletse kubwera kwa ine, pakuti ufumu wakumwamba ndi wa anthu amene ali ngati ana amenewa.”+ Luka 18:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Komabe Yesu anaitana anawo. Iye anati: “Alekeni anawo abwere kwa ine, musawaletse ayi. Pakuti ufumu wa Mulungu ndi wa anthu amene ali ngati ana amenewa.+ 1 Petulo 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Koma monga makanda obadwa kumene,+ muzilakalaka mkaka wosasukuluka+ umene uli m’mawu a Mulungu, kuti mwa kumwa mkakawo, mukule ndi kukhala oyenera chipulumutso,+
4 Chotero, aliyense amene adzadzichepetsa+ ngati mwana wamng’ono uyu ndi amene adzakhala wamkulu kwambiri mu ufumu wakumwamba.+
14 Koma Yesu anawauza kuti: “Alekeni anawo, ndipo musawaletse kubwera kwa ine, pakuti ufumu wakumwamba ndi wa anthu amene ali ngati ana amenewa.”+
16 Komabe Yesu anaitana anawo. Iye anati: “Alekeni anawo abwere kwa ine, musawaletse ayi. Pakuti ufumu wa Mulungu ndi wa anthu amene ali ngati ana amenewa.+
2 Koma monga makanda obadwa kumene,+ muzilakalaka mkaka wosasukuluka+ umene uli m’mawu a Mulungu, kuti mwa kumwa mkakawo, mukule ndi kukhala oyenera chipulumutso,+