Mateyu 20:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Tsopano pamene iwo anali kutuluka mu Yeriko,+ khamu lalikulu la anthu linam’tsatira. Luka 18:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Tsopano pamene anali kuyandikira ku Yeriko, munthu wina wakhungu anakhala pansi m’mphepete mwa msewu n’kumapemphapempha.+
35 Tsopano pamene anali kuyandikira ku Yeriko, munthu wina wakhungu anakhala pansi m’mphepete mwa msewu n’kumapemphapempha.+