Mateyu 20:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Tsopano pamene iwo anali kutuluka mu Yeriko,+ khamu lalikulu la anthu linam’tsatira. Maliko 10:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Kenako anafika mu Yeriko. Koma pamene iye ndi ophunzira ake ndi gulu lalikulu ndithu anali kutuluka mu Yeriko, Batimeyu, wopemphapempha komanso wakhungu (mwana wa Timeyu), anakhala pansi m’mphepete mwa msewu.+
46 Kenako anafika mu Yeriko. Koma pamene iye ndi ophunzira ake ndi gulu lalikulu ndithu anali kutuluka mu Yeriko, Batimeyu, wopemphapempha komanso wakhungu (mwana wa Timeyu), anakhala pansi m’mphepete mwa msewu.+