Maliko 10:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Kenako anafika mu Yeriko. Koma pamene iye ndi ophunzira ake ndi gulu lalikulu ndithu anali kutuluka mu Yeriko, Batimeyu, wopemphapempha komanso wakhungu (mwana wa Timeyu), anakhala pansi m’mphepete mwa msewu.+ Luka 18:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Tsopano pamene anali kuyandikira ku Yeriko, munthu wina wakhungu anakhala pansi m’mphepete mwa msewu n’kumapemphapempha.+
46 Kenako anafika mu Yeriko. Koma pamene iye ndi ophunzira ake ndi gulu lalikulu ndithu anali kutuluka mu Yeriko, Batimeyu, wopemphapempha komanso wakhungu (mwana wa Timeyu), anakhala pansi m’mphepete mwa msewu.+
35 Tsopano pamene anali kuyandikira ku Yeriko, munthu wina wakhungu anakhala pansi m’mphepete mwa msewu n’kumapemphapempha.+