Mateyu 22:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndiye tatiuzani, Mukuganiza bwanji? Kodi n’kololeka kupereka msonkho kwa Kaisara kapena ayi?”+ Luka 20:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kodi n’kololeka kuti ife tizipereka msonkho kwa Kaisara kapena ayi?”+