Mateyu 22:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Pakuti pouka kwa akufa, amuna sadzakwatira ndipo akazi sadzakwatiwa,+ koma adzakhala ngati angelo akumwamba. Luka 20:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Koma amene ayesedwa oyenerera+ kudzapeza moyo pa nthawi* imeneyo+ ndi kudzaukitsidwa kwa akufa+ sadzakwatira kapena kukwatiwa.
30 Pakuti pouka kwa akufa, amuna sadzakwatira ndipo akazi sadzakwatiwa,+ koma adzakhala ngati angelo akumwamba.
35 Koma amene ayesedwa oyenerera+ kudzapeza moyo pa nthawi* imeneyo+ ndi kudzaukitsidwa kwa akufa+ sadzakwatira kapena kukwatiwa.